-
Luka 11:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule, nanga otsatira anu amazitulutsa ndi mphamvu za ndani? Nʼchifukwa chake otsatira anuwo adzakuweruzani kuti ndinu olakwa.
-