-
Luka 11:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo ndipo ikalowa mkatimo imakhala mmenemo. Choncho zotsatira zake nʼzakuti zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.”
-