Luka 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamene gulu la anthulo linkachulukirachulukira, iye anayamba kunena kuti: “Mʼbadwo uwu ndi mʼbadwo woipa, ukufuna chizindikiro. Koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:29 Yesu—Ndi Njira, tsa. 176 Nsanja ya Olonda,8/15/1988, tsa. 8
29 Pamene gulu la anthulo linkachulukirachulukira, iye anayamba kunena kuti: “Mʼbadwo uwu ndi mʼbadwo woipa, ukufuna chizindikiro. Koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.+