-
Luka 11:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiye ngati thupi lako lonse ndi lowala kwambiri, popanda mbali ina yamdima, thupi lonse lidzawala kwambiri ngati mmene nyale imachitira pokuunikira ndi kuwala kwake.”
-