-
Luka 11:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Atalankhula zimenezi, Mfarisi wina anamupempha kuti akadye naye. Choncho iye anapita ndipo anakadya chakudya.