Luka 11:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma inu mukamapereka mphatso zachifundo,* muzipereka zinthuzo kuchokera pansi pamtima, mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 178 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 309/1/1988, tsa. 24
41 Koma inu mukamapereka mphatso zachifundo,* muzipereka zinthuzo kuchokera pansi pamtima, mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera.