Luka 11:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno iye anati: “Tsoka kwa inunso odziwa Chilamulo, chifukwa mumasenzetsa anthu katundu wovuta kunyamula, koma inuyo simukhudza katunduyo ngakhale ndi chala chanu!+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:46 Yesu—Ndi Njira, tsa. 178 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, ptsa. 24-25
46 Ndiyeno iye anati: “Tsoka kwa inunso odziwa Chilamulo, chifukwa mumasenzetsa anthu katundu wovuta kunyamula, koma inuyo simukhudza katunduyo ngakhale ndi chala chanu!+