Luka 11:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Mosakayikira, ndinu mboni pa zimene makolo anu anachita. Ndipo mukugwirizana ndi zimene anachitazo, chifukwa iwo anapha aneneri,+ pamene inu mukumanga manda awo.
48 Mosakayikira, ndinu mboni pa zimene makolo anu anachita. Ndipo mukugwirizana ndi zimene anachitazo, chifukwa iwo anapha aneneri,+ pamene inu mukumanga manda awo.