-
Luka 11:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Nʼchifukwa chake nzeru ya Mulungu inanenanso kuti: ‘Ndidzawatumizira aneneri ndi atumwi, koma iwo adzapha komanso kuzunza ena mwa iwo.
-