Luka 11:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Kuyambira magazi a Abele+ mpaka magazi a Zekariya, amene anaphedwa pakati pa guwa lansembe ndi nyumba yopatulika.’*+ Inde ndikukuuzani, mʼbadwo uwu udzayankha mlandu wa magazi amenewo. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:51 Yesu—Ndi Njira, tsa. 178 Nsanja ya Olonda,1/1/2013, tsa. 129/1/1988, ptsa. 24-25 Tsanzirani, tsa. 10
51 Kuyambira magazi a Abele+ mpaka magazi a Zekariya, amene anaphedwa pakati pa guwa lansembe ndi nyumba yopatulika.’*+ Inde ndikukuuzani, mʼbadwo uwu udzayankha mlandu wa magazi amenewo.
11:51 Yesu—Ndi Njira, tsa. 178 Nsanja ya Olonda,1/1/2013, tsa. 129/1/1988, ptsa. 24-25 Tsanzirani, tsa. 10