Luka 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyi, chigulu cha anthu masauzande ambirimbiri chinasonkhana, moti ankapondanapondana. Ndiyeno Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi zofufumitsa za Afarisi, zimene ndi chinyengo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 180 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 8
12 Pa nthawiyi, chigulu cha anthu masauzande ambirimbiri chinasonkhana, moti ankapondanapondana. Ndiyeno Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi zofufumitsa za Afarisi, zimene ndi chinyengo.+