Luka 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso ndikukuuzani mabwenzi anga,+ musamaope amene amapha thupi lokha, omwe sangathe kuchita zoposa pamenepa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,7/2018, tsa. 5
4 Komanso ndikukuuzani mabwenzi anga,+ musamaope amene amapha thupi lokha, omwe sangathe kuchita zoposa pamenepa.+