Luka 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo aliyense amene wanena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma aliyense amene wanyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa.+
10 Ndipo aliyense amene wanena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma aliyense amene wanyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa.+