Luka 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho siyani kudera nkhawa kuti mudzadya chiyani komanso kuti mudzamwa chiyani ndipo siyani kuvutika mumtima.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, ptsa. 16-19
29 Choncho siyani kudera nkhawa kuti mudzadya chiyani komanso kuti mudzamwa chiyani ndipo siyani kuvutika mumtima.+