Luka 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina mʼdzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti inuyo mumafunikira zinthu zonsezi.+
30 Chifukwa zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina mʼdzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti inuyo mumafunikira zinthu zonsezi.+