Luka 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulitsani zinthu zanu nʼkupereka mphatso zachifundo.*+ Pangani zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene akuba sangafikeko komanso njenjete* sizingawononge. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 181 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 8
33 Gulitsani zinthu zanu nʼkupereka mphatso zachifundo.*+ Pangani zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene akuba sangafikeko komanso njenjete* sizingawononge.