-
Luka 12:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 mbuye wa kapoloyo adzabwera pa tsiku limene iye sakuyembekezera ndi pa ola limene sakulidziwa, ndipo adzamupatsa chilango choopsa nʼkumupatsa gawo, limodzi ndi anthu osakhulupirika.
-