Luka 12:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndiyeno kapolo ameneyo, amene anadziwa zimene mbuye wake ankafuna koma osakonzekera kubwera kwake kapena kuchita zimene anamuuza,* adzakwapulidwa zikoti zambiri.+
47 Ndiyeno kapolo ameneyo, amene anadziwa zimene mbuye wake ankafuna koma osakonzekera kubwera kwake kapena kuchita zimene anamuuza,* adzakwapulidwa zikoti zambiri.+