-
Luka 12:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Chifukwa kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, mʼnyumba imodzi mudzakhala anthu 5 osemphana maganizo, atatu kutsutsana ndi awiri, awiri kutsutsana ndi atatu.
-