-
Luka 13:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Nanga bwanji za anthu 18 aja, amene nsanja inawagwera ku Siloamu nʼkuwapha? Kodi mukuganiza kuti anali ochimwa kwambiri kuposa anthu onse amene akukhala mu Yerusalemu?
-