Luka 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mtengo wamkuyu mʼmunda wake wa mpesa, ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo, koma sanapezemo chilichonse.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:6 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 184-185 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, ptsa. 25-2610/15/1988, tsa. 8
6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mtengo wamkuyu mʼmunda wake wa mpesa, ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo, koma sanapezemo chilichonse.+