-
Luka 13:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno anauza munthu wosamalira munda wa mpesawo kuti, ‘Kwa zaka zitatu tsopano ndakhala ndikubwera kudzafuna nkhuyu mumtengowu, koma sindinapezemo ngakhale imodzi. Uduleni mtengo umenewu! Nʼchifukwa chiyani ukungowononga nthaka?’
-