-
Luka 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Wosamalira mundayo anayankha kuti, ‘Mbuyanga, bwanji muusiye chaka chino chokha. Ine ndikumba kuzungulira mtengowu nʼkuthirapo manyowa.
-