Luka 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mmenemo munali mayi wina amene mzimu woipa* unamudwalitsa kwa zaka 18. Iye anali wopindika msana moti sankatha kuweramuka. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Yesu—Ndi Njira, tsa. 185 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, ptsa. 8-9
11 Mmenemo munali mayi wina amene mzimu woipa* unamudwalitsa kwa zaka 18. Iye anali wopindika msana moti sankatha kuweramuka.