Luka 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yesu atamuona, analankhula naye nʼkumuuza kuti: “Mayi, mwamasuka ku matenda anu.”+