Luka 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Ambuye anamuyankha kuti: “Achinyengo inu,+ kodi aliyense wa inu samasula ngʼombe yake kapena bulu wake mʼkhola pa Sabata nʼkupita naye kukamumwetsa madzi?+
15 Koma Ambuye anamuyankha kuti: “Achinyengo inu,+ kodi aliyense wa inu samasula ngʼombe yake kapena bulu wake mʼkhola pa Sabata nʼkupita naye kukamumwetsa madzi?+