Luka 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uli ngati kanjere ka mpiru* kamene munthu anakatenga nʼkukadzala mʼmunda wake. Kenako kanamera nʼkukhala mtengo, moti mbalame zamumlengalenga zinamanga zisa munthambi zake.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:19 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, ptsa. 17-19, 21
19 Uli ngati kanjere ka mpiru* kamene munthu anakatenga nʼkukadzala mʼmunda wake. Kenako kanamera nʼkukhala mtengo, moti mbalame zamumlengalenga zinamanga zisa munthambi zake.”+