Luka 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Uli ngati zofufumitsa zimene mayi wina anazitenga nʼkuzisakaniza ndi ufa wokwana mbale zitatu zazikulu zoyezera,* moti mtanda wonsewo unafufuma.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, ptsa. 19-21
21 Uli ngati zofufumitsa zimene mayi wina anazitenga nʼkuzisakaniza ndi ufa wokwana mbale zitatu zazikulu zoyezera,* moti mtanda wonsewo unafufuma.”+