-
Luka 13:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno munthu wina anamufunsa kuti: “Ambuye, kodi nʼzoona kuti anthu amene adzapulumuke ndi ochepa?” Iye anawauza kuti:
-