Luka 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwininyumba akadzanyamuka nʼkukiya chitseko, inu mudzaima panja nʼkumagogoda chitsekocho, ndipo mudzanena kuti, ‘Ambuye titsegulireni.’+ Koma iye adzakuyankhani kuti: ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera.’ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:25 Yesu—Ndi Njira, tsa. 192 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, tsa. 81/15/1986, tsa. 11
25 Mwininyumba akadzanyamuka nʼkukiya chitseko, inu mudzaima panja nʼkumagogoda chitsekocho, ndipo mudzanena kuti, ‘Ambuye titsegulireni.’+ Koma iye adzakuyankhani kuti: ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera.’