-
Luka 13:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma iye adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera. Chokani pamaso panga, inu nonse ochita zinthu zosalungama!’
-