Luka 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe ndiyenera kupitiriza ulendo wanga lero ndi mawa ndi tsiku linalo, chifukwa nʼkosayenera kuti mneneri amuphere kunja kwa Yerusalemu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 193 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, tsa. 9
33 Komabe ndiyenera kupitiriza ulendo wanga lero ndi mawa ndi tsiku linalo, chifukwa nʼkosayenera kuti mneneri amuphere kunja kwa Yerusalemu.+