-
Luka 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiye amene anakuitanani uja angabwere nʼkudzakuuza kuti, ‘Choka pamenepa pakhale bambo awa.’ Zikatero ungachokepo mwamanyazi nʼkukakhala kumapeto kwenikweni.
-