Luka 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni, kuti munthu amene anakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Zikadzatero udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 311/15/1989, tsa. 25
10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni, kuti munthu amene anakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Zikadzatero udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+