Luka 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ukatero udzakhala wosangalala chifukwa alibe choti adzakubwezere. Mulungu adzakubwezera anthu olungama akamadzaukitsidwa.”+
14 Ukatero udzakhala wosangalala chifukwa alibe choti adzakubwezere. Mulungu adzakubwezera anthu olungama akamadzaukitsidwa.”+