Luka 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma onse anayamba kupereka zifukwa zokanira.+ Woyamba anamuuza kuti, ‘Ine ndagula munda ndipo ndikuyenera kupita kukauona. Pepani sinditha kubwera.’ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:18 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 194-195 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 8-9
18 Koma onse anayamba kupereka zifukwa zokanira.+ Woyamba anamuuza kuti, ‘Ine ndagula munda ndipo ndikuyenera kupita kukauona. Pepani sinditha kubwera.’