Luka 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno mbuye uja anauza kapolo wakeyo kuti, ‘Pita mʼmisewu ina yakunja kwa mzinda ndipo ukalimbikitse anthu abwere kuno kuti nyumba yanga idzaze.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:23 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 194-195 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 9
23 Ndiyeno mbuye uja anauza kapolo wakeyo kuti, ‘Pita mʼmisewu ina yakunja kwa mzinda ndipo ukalimbikitse anthu abwere kuno kuti nyumba yanga idzaze.+