-
Luka 14:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Mwachitsanzo, ndi ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja sayamba wakhala pansi nʼkuwerengera ndalama zimene adzawononge, kuti aone ngati ali ndi ndalama zokwanira kumalizira nsanjayo?
-