-
Luka 14:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Kapena ndi mfumu iti, imene popita kukakumana ndi mfumu inzake kunkhondo, siyamba yakhala pansi nʼkuganizira mofatsa ngati asilikali ake 10,000 angathe kulimbana ndi asilikali 20,000 a mfumu imene ikubwera kudzalimbana naye?
-