Luka 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndi wosayenera kuuthira munthaka kapena mʼmanyowa. Anthu amangoutaya kunja. Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:35 Yesu—Ndi Njira, tsa. 197 Nsanja ya Olonda,1/1/1989, tsa. 9
35 Ndi wosayenera kuuthira munthaka kapena mʼmanyowa. Anthu amangoutaya kunja. Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+