Luka 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akafika kunyumba amasonkhanitsa anzake ndi anthu oyandikana naye nyumba nʼkuwauza kuti, ‘Sangalalani limodzi ndi ine, chifukwa ndapeza nkhosa yanga imene inasowa ija.’+
6 Akafika kunyumba amasonkhanitsa anzake ndi anthu oyandikana naye nyumba nʼkuwauza kuti, ‘Sangalalani limodzi ndi ine, chifukwa ndapeza nkhosa yanga imene inasowa ija.’+