Luka 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kapena ndi mayi uti amene ali ndi ndalama zokwana madalakima 10,* ndiye imodzi itamutayika, sangayatse nyale ndi kusesa mʼnyumba nʼkuifufuza mosamala mpaka ataipeza? Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2020, ptsa. 24-25 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2242 Nsanja ya Olonda,12/1/2012, tsa. 212/1/2003, ptsa. 14-15, 17-18
8 Kapena ndi mayi uti amene ali ndi ndalama zokwana madalakima 10,* ndiye imodzi itamutayika, sangayatse nyale ndi kusesa mʼnyumba nʼkuifufuza mosamala mpaka ataipeza?
15:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2020, ptsa. 24-25 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2242 Nsanja ya Olonda,12/1/2012, tsa. 212/1/2003, ptsa. 14-15, 17-18