Luka 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo akaipeza amasonkhanitsa anzake* komanso anthu oyandikana nawo nyumba nʼkuwauza kuti, ‘Sangalalani limodzi ndi ine, chifukwa ndapeza khobidi la dalakima* limene linanditayika lija.’
9 Ndipo akaipeza amasonkhanitsa anzake* komanso anthu oyandikana nawo nyumba nʼkuwauza kuti, ‘Sangalalani limodzi ndi ine, chifukwa ndapeza khobidi la dalakima* limene linanditayika lija.’