-
Luka 15:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Wamngʼono anapempha bambo ake kuti, ‘Bambo, mundipatsiretu cholowa changa pa chuma chanuchi.’ Choncho bambowo anagawa chuma chawocho kwa anawo.
-