-
Luka 15:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Patangopita masiku owerengeka, mwana wamngʼono uja anasonkhanitsa zinthu zake zonse nʼkupita kudziko lina lakutali. Kumeneko anayamba kukhala moyo wotayilira ndipo anasakaza chuma chake chonse.
-