Luka 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho ananyamukadi nʼkupita kwa bambo ake. Ali chapatali ndithu, bambo akewo anamuona ndipo anagwidwa ndi chifundo. Kenako anamuthamangira nʼkumukumbatira ndipo anamukisa* mwachikondi. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:20 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 201-202 Bwererani kwa Yehova, tsa. 10 Nsanja ya Olonda,10/1/1998, ptsa. 12-132/15/1989, tsa. 162/1/1989, tsa. 81/15/1988, ptsa. 21, 23
20 Choncho ananyamukadi nʼkupita kwa bambo ake. Ali chapatali ndithu, bambo akewo anamuona ndipo anagwidwa ndi chifundo. Kenako anamuthamangira nʼkumukumbatira ndipo anamukisa* mwachikondi.
15:20 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 201-202 Bwererani kwa Yehova, tsa. 10 Nsanja ya Olonda,10/1/1998, ptsa. 12-132/15/1989, tsa. 162/1/1989, tsa. 81/15/1988, ptsa. 21, 23