-
Luka 15:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma bambowo anauza akapolo ake kuti, ‘Fulumirani, tengani mkanjo wabwino kwambiri uja mumuveke. Mumuvekenso mphete kudzanja lake ndi nsapato kumapazi kwake.
-