-
Luka 15:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Koma mwana wamkulu anali kumunda. Ndiyeno pamene ankabwerera nʼkuyandikira kunyumbako, anamva phokoso la nyimbo komanso anthu akuvina.
-