Luka 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anamuuza kuti, ‘Mngʼono wanu wabwera ndipo bambo anu amuphera mwana wa ngʼombe wonenepa, chifukwa amulandira ali bwinobwino.’*
27 Iye anamuuza kuti, ‘Mngʼono wanu wabwera ndipo bambo anu amuphera mwana wa ngʼombe wonenepa, chifukwa amulandira ali bwinobwino.’*