-
Luka 15:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Poyankha iye anauza bambo akewo kuti, ‘Zaka zonsezi ine ndakhala ndikukugwirirani ntchito ngati kapolo ndipo sindinaphwanyepo malamulo anu nʼkamodzi komwe. Koma simunandipatseko ngakhale kamwana ka mbuzi kuti ndisangalale ndi anzanga.
-